Last time tinacheza naye artist ameneyu linali Saturday last week

Last time tinacheza naye artist ameneyu linali Saturday last week.
Iye anatitumizila nyimbo kuti tiyimvere koma tisayipange kaye upload. Titayimvera nyimboyo tinamuyimbila kumupanga recommend kuti alibho ayituluse osadziwa kuti inali last track yake yomaliza kutulusa.
Lero tangomva kuti wazimpha chifukwa chimene waziphela sitikuchiziwa.
Rest in peace Ipenchimphapa 🕊️

Comment Here