Major-General-Khalen-Ft-Space-Dear-Mama
*RELYCs for Dear Mama*
yeah
break up is nothing
just imagine pushing life without without father
dem dear mama ulendo wanga ndi oyenda ndi ntima ngakhale pena zikavuta ndienda mu m’dima
koma ndikudziwa kut ndikafika chifukwa sindiyima
m’manja mwanga muli kalata yodzadza ndimafuso
Dear ma ndayambapo kod ndi ulendo wanji osabwelela chonsecho ndiulendo wawufupi fans imayenda maulendo ataliatali kumakafika overseas koma inu lelo ama sizii
ulendo wanu wama yatd ten koma pano mukutha zaka ten
Ama ndamaliza ma pen ten kulembela makalata kwa inu koma osayankhidwa mama one thing you should know
no matter how old i can be olo ine nditamela invii
sindingakuyiwalen ama
olo ndili ndi ndrama daily kudya nyama.
Amama amama ah ndilila
amama amama ine ndilila
amama amama ah ndilila Amama × 3
Dear mama munandisiya wachichepele
movutika momwemo ndakula ndi achina tupele
komabe naye Mulungu mphavu zake sizinachepele lelo ndine
abambo bambo kulitu ya china Raheem ama zidzukulu ndi plenty koma daily zimandifusa mafuso twenty kod agogo alikut ? ine mu ntima kut dii!!!!!
its only one thing that brings me back always
the memories kills me
koma ndikudziwa ama muliku heaven tidzabwela konko ife ku heaven tidzakhala limodzi monga banja mu eden ndi zidzukulu zanu
inuyo eleven tsono nono
ine life ya m’ma thalaven
ndicholinga Mulungu andi save ine pamodzi ndi seven moyo wanga ndaupeleka ah nsembe ine
moyo wanga naupeleka nsembe ine
moyo wanga ndaupeleka ah nsembe ine
Amama amama ah ndilila
Amama amama ine ndilila amama amama ah
ndilila Amama × 4
Comment Here