Spread the love
Maji Yachita thipiwa Episode 3

Maji Yachita thipiwa Episode 3

Episode 3 ¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶   Mu Part 2 tinasiila pomwe sir Bern anadabwa za zomwe zimachita mkalasi muja.   Tipitilize   Sir Bern anaphunzitsa bwino ndipo ana onse anamva.Ndipo anapeleka ntchito koma Sammie sanalembe. Kwa masiku angapo  Sammie wakhala akuzunzika maka ndi Eliza komanso anzake aja.   Ngati mukukumbukila Ku part 1 tinaonako Grace yemwe nthawi >>>>
Maji Yachita thiphwa Epsode 2

Maji Yachita thiphwa Epsode 2

Epsode 2 ¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶ Mu part 1 tinasiila pomwe Sammie anali atakanidwa ndipo mbiri yawanda. Tipitilize Tsiku linali lolemba pomwe Sammie anali akudzimvera chisoni chifukwa mbiri inali itawanda moipa. Sammie atangolowa mkalasi oyamba kuyankhula anali Eliza. Eeee koma amuna ena ngogwetsa ulesi mwamva inu..Hmmm…anayamba choncho Eliza. Ndipo Jimmy sanachedwe kuyankha… Kodi Eliza ukuti bwanji? Eeee adha >>>>
Maji yachita thiphwa Epsode 1

Maji yachita thiphwa Epsode 1

Episode 1 Hahahahahaha iwe Sammie taziyang’ane nde undiyang’ane then uganize statement yako wakambayo…are you serious? Hannah please kulola kapena kundikana zili mmanja mwako.. koma chonde usandinyoze choncho.. Sammie wazinyozetsa wekha,unatani osakapeza ananyoni uko omwe mungafanane type…Nde undimvetse…pa school ponse pano olo mwana wa form 1 sangakulore.Mkazi amafuna mamuna oti atha kumamuthandiza.Iweyo ungathandize ndani? Ndakumva Hannah >>>>
MR. TEACHER (1)

MR. TEACHER (1)

Read the full story below I was nicknamed Seal-breaker by my friends. Why? Because not only was I an expert in breaking virginity, I had deflowered so many girls. Why do I like virgins, I know not but I know having the knowledge that a girl was a virgin was a serious turn on for >>>>