Toriah-Birimankhwe

*Toriah drops “Birimankhwe”*
Toriah has released her highly anticipated single “Birimankhwe”.
Produced by Dru at Janta’s SU Records, the song drops today, Friday, 21st August 2020.
*Birimankhwe Lyrics*
[Intro];
Yeah, people these days change like Chameleons you know. They change, depending on where they are…. (((((Toriah)))))
(Verse 1);
Ndinafera mawanga ankhanga/ Ndinkati ndapeza mzanga/ Kumuwonetsa kwa amzanga/ Osadziwa ndikudziyika ndekha pa Minga eeeeh/
Yeah i know Nobody is perfect// Nane ndiri ndi zofowoka//
Ndife anthu, sife nyama, ndichifukwa chake tinkakhala kukambirana//
Mtima wamzako ndi tsidya lina aaah// Ukamupepesa ati Nkhani yatha aaah// Osadziwa akusunguira adha, Nkhonya yobwezera imawawa sananame aja//
(Hook);
Munthu ndi Birimankhwe/ Munthudi amasintha aaaaah///
Munthu ndi Birimankhwe, amasintha kutengera ndipomwe wafikapo// X2….
(Verse 2);
Sindinakwatire ndi chi Messi ine/ Sindinakwatire ndi chi Ronaldo/ Zomandiyenda Njomba ine ayi, ndatopa kukhalira kumwa Panado//
Ndatiii, Sindinakwatire ndi chi Under taker, sindinakwatire ndi chi John Cena//
Ngati watopa nane peza wina/ Mwina nanenso ndingawone zina//
Banja ndinalifuna, koma bambowa kumenya//
Dziko lake lomweri, koma ngati ndiri ku Kenya//
Asawone chinthu, pompopompo kundikwenya//
Sonu Nthena, nilolani niyendepo apa//
((((((((Back to chorus))))))))
(Verse 3)
Ndikanakonda nkanakhala ine, nanu mpaka kale//
Koma Zawonjeza, ndichani ndinalakwa ineee//
Tachokadi kutali bambo a Juh, koma tisiyane// Ndikanakonda ndikanakhala, ndikanakhala, nanu Mpaka kale//////
((((((Back to Chorus(hook))))))))))))))))))))))))))))))))))))

Comment Here