HomeEntertainmentMusicEkelly-Cholera-prod-by-multskillzlab Ekelly-Cholera-prod-by-multskillzlab April 27, 2023April 27, 2023 Comment Here
Amalawi anzanga, tiyeni titsate njila mwanvanzi kuti tipewe cholera ndi thenda yotetezeka kwambili. Tiyeni tigonjetse cholera m’malawi. Reply
Tiyeni tigonjetse cholera amalawi. Nthenda imeneyi ndi yoopsa komano ndiyochizika👏👏
Amalawi anzanga, tiyeni titsate njila mwanvanzi kuti tipewe cholera ndi thenda yotetezeka kwambili. Tiyeni tigonjetse cholera m’malawi.