PHYZIX PARTNERS WITH GIBO PEARSON IN “CHEKERA” Malawi hip hop icon, Phyzix, has collaborated with fastest faming artist, Gibo Pearson, in a new track titled Chekera. The Cholapitsa king, Phyzix, has announced about the big project through his social madia pages, adding that it will be released on 10th April 2023. Barely days after Gibo […]Read More
Last time tinacheza naye artist ameneyu linali Saturday last week. Iye anatitumizila nyimbo kuti tiyimvere koma tisayipange kaye upload. Titayimvera nyimboyo tinamuyimbila kumupanga recommend kuti alibho ayituluse osadziwa kuti inali last track yake yomaliza kutulusa. Lero tangomva kuti wazimpha chifukwa chimene waziphela sitikuchiziwa. Rest in peace Ipenchimphapa 🕊️Read More

