Tags : Clem-J

Articles

Clem J Drops Banger

MAN CRUSH MONDAY Clem J Clem J ndi artist oti kupanda kusamala nae atha kubudula ndiwo za gulu chifukwa sound yomwe akuyika ndiyachabe heavy. Tamvelani tracks watulusa chapompanoyi titled “Sesana” ndipowe mudziwe kuti kumalawi kuno kuli luso🙌 Sesana ndi track yomwe ili mu Ep yake yomwe ituluke anytime from now. Stream and download SESANA a […]Read More