Clem J Drops Banger

 Clem J Drops Banger

MAN CRUSH MONDAY

Clem J

Clem J ndi artist oti kupanda kusamala nae atha kubudula ndiwo za gulu chifukwa sound yomwe akuyika ndiyachabe heavy. Tamvelani tracks watulusa chapompanoyi titled “Sesana” ndipowe mudziwe kuti kumalawi kuno kuli luso🙌

Sesana ndi track yomwe ili mu Ep yake yomwe ituluke anytime from now.

Stream and download SESANA a song by Clem J here:https://goldencitytower.com/clem-j-sesana-prod-by-tommybeats/

download more music @ www.goldencitytower.com

Golden city tower entertainment

Digiqole ad

Comment Here

Related post

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *